Matayo 15:18-19

Matayo 15:18-19 NTNYBL2025

Nambho chindhu icho chituluka mkamwa chichoka mumtima, chimenecho nde icho chimchita mundhu siwadavomelezeka pakumlambila Mnungu. Pakuti mumtima yachoka maganizo ya kupha, chigololo, uhule, unami, kuba, umboni wanthila ni matukwano.