Matayo 14:28-29
Matayo 14:28-29 NTNYBL2025
Petulo wadamkambila, “Ambuye, ngati nde imwe, nikambileni nikuchateni pakuyenda pa mwamba pa majhi.” Yesu wadamkambila, “Chabwino, majha.” Ndiipo Petulo wadachika mbwato waukulu, wadayenda pamwamba pa majhi ni kumpitila Yesu.