Matayo 12
12
Nghani za siku Lopumulila
Maluko 2:23-28; Luka 6:1-5
1Ndhawi imeneyo, Yesu wamapita mminda ya mapila siku Lopumulila. Ndiipo oyaluzidwa wake adavela njala, adayamba kupulula ni kufikisa njele za mapila ni kudya. 2Afalisayo yapo adaona chimwecho, adamkambila Yesu, “Penya, woyaluzidwa wako achita vosaloledwa kuchita Musiku Lopumulila.”
3Yesu wadayangha, “Bwanji, simudasome ivo wadachita Daudi ni achanjake yapo adali ni njala? 4Iye ni achanjake adalowa Mnyumba ya Mnungu, adadya mabumunda yayo yadachochedwa kwa Mnungu. Iye ni achanjake saadalolezedwe nambho yawo adafunika kudya mabumunda yajha ni ajhukulupe. 5Simudasome chikalakala cha thauko kuti ajhukulu wakulu awananga thauko pa Siku Lopumulila kwakuchita yajha siyafunika, nambho sadaonekane kuti wolakwa? 6Chipano nikukambilani, pano wali wamkulu kupitilila Nyumba ya Mnungu. 7Ngati mdakajhiwa mate ya malembo yaya, ‘Nifuna kulengelena lisungu, osati njhembe yo pyeleza,’ simdakalamula wandhu wosalakwa. 8Pakuti Mwana wa Mundhu nde Mbuye wa Siku Lopumulila.”
Yesu wamlamicha Mundhu ovuwala jhanja
Maluko 3:1-6; Luka 6:6-11
9Yesu wadachokapo pamalo yajha ni kulowa mnyumba yokomanilana Ayahudi. 10Mmenemo mdali ni mundhu mmojhi wavulala jhanja. Ndiipo Afalisayo wina adamfunjha Yesu, “Bwanji, ni bwino kumlamicha mundhu Siku Lopumulila?” Adamfunjha chimwecho kuti apate ndande yakumgwilila.
11Yesu wadaakambila, “Tikambe mmojhi wanu wali ni mbelele iyo yabila mjhenje lonyowa, bwanji siwaichuula mujha mjhenje Siku Lopumulila? 12Mundhu wali mbasa kupitilila mbelele! Chimwecho tifunika kuchita vindhu vabwino pa Siku Lopumulila.” 13Ndiipo Yesu wadamkambila yujha mundhu, “Tambasula jhanja lako.”
Wadatambasula, nalo lidalama ni kukhala ngati jhanja lina lijha. 14Basi Afalisayo adatuluka kubwalo, ndiipo adafunafuna ndande ya kumphela Yesu.
Mbowa uyo wasanghidwa ni Mnungu
15Yesu yapo wadajhiwa chindhu chimenecho, wadachoka pamalo pajha. Wandhu ambili adamchata, niiye wadalamicha wandhu wonjhe yawo adali odwala, 16ndiipo wadalamula kuti sadaakambila wandhu nghani zake. 17Wadachita chimwecho kuti chijha wadachikamba mlosi Isaya chikwanile,
18“Uyu nde mbowa wanga uyo namsangha,
uyo nimkonda nikondwelechedwa nayo.
Siniike mzimu wanga mkati mwake,
iye siwalalikile wandhu a mayiko yonjhe lamulo langa.
19Siwayambana kapina kubula phokoso,
palibe mundhu uyo siwauvele mvekelo wake mnjila.
20Njhungwi iyo yapindika siwaityola,
wala nyali yofuka mauchi siwaithima,
mbaka kila mundhu walamulidwe ngati umo ifunukila.
21Wandhu a mayiko yonjhe samkhulupilile iye.”
Yesu ni Belizebuli
Maluko 3:20-30; Luka 11:14-23
22Ndiipo wandhu adampelekela Yesu mundhu osapenya ni uyo siwakhoza kukamba, ndande wadazamwa ni chiwanda. Yesu wadamlamicha, wadakhoza kukamba ni kupenya. 23Wandhu wonjhe adadabwa ni adakamba, “Bwanji, uyu osati Mwana wa Daudi?”
24Nambho Afalisayo yapo adavela yameneyo, adakamba, “Mundhu uyu wachocha viwanda kwa mbhavu za Belizebuli, wamkulu wa viwanda.”
25Yesu wadajhiwa maganizo yao, wadakambila, “Ufumu uliwonjhe ukabulana ni ukapatukana magulumagulu, ufumu umenewo siukhoza kulimba. Jhiko kapina wandhu a nyumba imojhi apatukana achinawene magulumagulu yayo yachuchana, nyumba imeneyo siikhoza kulimba. 26Ngati Satana wamtopola Satana mnjake mmeneyo wajhipatula mwene wake magulumagulu, chimwecho ufumu wake siuime bwanji? 27Anyiimwe mkamba nichocha chiwanda kwa mbhavu za Belizebuli, bwanji, wana wanu achocha viwanda kwa mbhavu zayani? Kwa ndande imeneyo, achiwanawanu saakulamuleni. 28Nambho ngati nichocha viwanda kwa mbhavu ya Mzimu wa Mnungu, mujhiwe kuti Ufumu wa Mnungu wathofika kwanu.”
29“Palibe mundhu uyo wakhoza kulowa mnyumba ya mundhu uyo wali ni mbhavu ni kumlanda chuma chake, mbaka poyamba wammange mundhu wa mbhavu yujha. Pamenepo nde yapo siwakhoze kumlanda chuma chake.”
30“Mundhu walionjhe uyo siwali pamojhi ni ine wanichucha ni walionjhe uyo wakana kukusa pamojhi ni ine, mmeneyo watomwaza. 31Chimwecho nikukambilani, volakwa vonjhe ni chipongwe avichita wandhu saalekeleledwe, nambho yao amchitala chipongwe Mzimu Woyela saalekeleledwa machimo yao. 32Walionjhe uyo wamtukwana Mwana wa Mundhu siwalekeleledwe, nambho uyo wamtukwana Mzimu Woyela, siwalekeleledwa, kuyambila ndhawi ino mbaka ndhawi ikujha.”
Mtengo ni vipacho vake
Luka 6:43-45
33“Mtengo wabwino ubala vipacho vabwino, ni mtengo waopa ubala vipacho voipa. Pakuti mtengo ujhiwika pa vipacho vake. 34Anyiimwe muli woipa ngati njoka zili ni sumu! Mkhoza bwanji kukamba vindhu vabwino ikakhala mwachinawene wake woipa? Pakuti mundhu wakamba yajha yajhala mumtima mwake. 35Mundhu wabwino wachocha vindhu vabwino vali mumtima mwake ni mundhu woipa wachocha vindhu voyipa vali mumtima mwake.”
36“Zenedi Nikukambilani, siku la lamulo wandhu siafunike wakambe pa kila mawu loipa ilo alikamba. 37Pakuti kwa mawu yako siuvomelezeke kuti ni wabwino, ni kwa mawu yako siulamulidwe kuti ni woipa.”
Wandhu afuna vizindikilo
Maluko 8:11-12; Luka 11:29-32
38Ndiipo akumojhi wa oyaluza athauko ni akumojhi a Afalisayo adamkambila Yesu, “Oyaluza, tifuna tione chizindikilo kuchokela kwanu.”
39Yesu wadaayangha, “Mbadwa woipa ni icho chilibe chikhulupililo! Mfuna chizindikilo, nambho simpachidwa chizindikilo nambho chizindikililo chijha cha mlosi Yona. 40Yona wadakhala masiku ya tatu usiku ni usana mmimba mwa njhomba, nde umo Mwana wa Mundhu siwakhale mkati mwa ndhaka masiku ya tatu usiku ni usana. 41Wandhu akumujhi wa Ninawi siku la lamulo siaime ni kukupachani mlandu anyiimwe kuti niwolakwa. Pakuti a Ninawi adalapa ndande ya ulaliki wa Yona, chimwecho yapa kuli wamkulu kupitilila Yona! 42Mfumukazi wa ku Sheba siwaime ndhawi ya lamulo niiye siwakukwilizileni anyiimwe kuti ni wolakwa. Pakuti iye wadamanga ulendo kuchokela mjhiko lake kujha kuvela mawu ya njelu ya Solomoni, ni pano walipo wamkulu kupitilila Solomoni!”
Kubwela kwa chiwanda
Luka 11:24-26
43“Chiwanda chikamchoka mundhu, chizungulila pamalo youma kufunafuna malo yopumulila, ningati sichipata malo, 44chijhikambila chene, ‘Nibwelele ku nyumba kwanga uko nachoka.’ Nambho pajha chibwela nikuipeza nyumba yopande kandhu, yalambulidwa ni kila chindhu chaikidwa bwino, 45wachoka ni kupita kutenga viwanda vina saba, voipa kupitilila icho ni wonjhe akujha kumlowa ni kukhala mmememo. Chimwecho umoyo wa mundhu yujha ukhala woipa kupitilila poyamba. Ndeumo siikhalile kwa mbadwa uwu woipa.”
Achabale ni amae auzene a Yesu
Maluko 3:31-35; Luka 8:19-21
46Yesu yapo wadali wakali kukambana ni gulu la wandhu, maye wake ni achabale wake adajha ni kuima kubwalo, naafuna kukamba nayo. 47Ndiipo mundhu mmojhi wadamkambila, “Maye wako ni achabale wako ali kubwalo, afuna kukambana ni iwe.”
48Yesu wadamuyangha mundhuyo, “Maye wanga ni ayani? Ni achabale wanga ni achiyani?” 49Ndiipo wadatambasulila jhanja lake ni kwaalangizila oyaluzidwa wake, ni wakamba, “Anyiyawa nde maye wanga ni achabale wanga! 50Walionjhe uyo wachita vijha avifuna Atate wanga ali kumwamba, mmeneyo nde mbale wanga, ni mlongo wanga ni maye wanga.”
Actualmente seleccionado:
Matayo 12: NTNYBL2025
Destacar
Compartir
Copiar

¿Quieres tener guardados todos tus destacados en todos tus dispositivos? Regístrate o inicia sesión
The New Testament in Nyanja @The Word for The World International and Nyanja Language translation, 2025. All rights reserved.

: