Matayo 1:20
Matayo 1:20 NTNYBL2025
Yusufu yapo wamaganizila chindhu ichi, Mtumiki wa kumwamba wa Ambuye wadamjhela kumaloto kumkambila Yusufu mwana wa Daudi, Usadaopa kumtenga Maliya kukhala mkazako pakuti pathupi pake pajha kwa mbhavu za Mzimu Woyela.