1
MACHITIDWE A ATUMWI 7:59-60
Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014
BLPB2014
Ndipo anamponya miyala Stefano, alikuitana Ambuye, ndi kunena, Ambuye Yesu, landirani mzimu wanga. Ndipo m'mene anagwada pansi, anafuula ndi mau akulu, Ambuye, musawaikire iwo tchimo ili. Ndipo m'mene adanena ichi, anagona tulo.
Comparar
Explorar MACHITIDWE A ATUMWI 7:59-60
2
MACHITIDWE A ATUMWI 7:49
Thambo la kumwamba ndilo mpando wachifumu wanga, ndi dziko lapansi chopondapo mapazi anga. Mudzandimangira nyumba yotani, ati Ambuye, kapena malo a mpumulo wanga ndi otani?
Explorar MACHITIDWE A ATUMWI 7:49
3
MACHITIDWE A ATUMWI 7:57-58
Koma anafuula ndi mau akulu, natseka m'makutu mwao, namgumukira iye ndi mtima umodzi; ndipo anamtaya kunja kwa mudzi, namponya miyala; ndipo mbonizo zinaika zovala zao pa mapazi a mnyamata dzina lake Saulo.
Explorar MACHITIDWE A ATUMWI 7:57-58
Inicio
Biblia
Planes
Vídeos