1
MACHITIDWE A ATUMWI 6:3-4
Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014
BLPB2014
Chifukwa chake, abale, yang'anani mwa inu amuna asanu ndi awiri a mbiri yabwino, odzala ndi Mzimu ndi nzeru, amene tikawaike asunge ntchito iyi. Koma ife tidzalimbika m'kupemphera, ndi kutumikira mau.
Comparar
Explorar MACHITIDWE A ATUMWI 6:3-4
2
MACHITIDWE A ATUMWI 6:7
Ndipo mau a Mulungu anakula; ndipo chiwerengero cha ophunzira chidachulukatu ku Yerusalemu; ndipo khamu lalikulu la ansembe linamvera chikhulupirirocho.
Explorar MACHITIDWE A ATUMWI 6:7
Inicio
Biblia
Planes
Vídeos