Logo YouVersion
Ikona vyhledávání

EKSODO 31:2-5

EKSODO 31:2-5 BLPB2014

Taona ndaitana ndi kumtchula dzina lake, Bezalele, mwana wa Uri, mwana wa Huri, wa fuko la Yuda; ndipo ndamdzaza ndi mzimu wa Mulungu, ndi luso, ndi nzeru, ndi chidziwitso, ndi m'ntchito zilizonse, kulingirira ntchito zaluso, kuchita ndi golide ndi siliva ndi mkuwa, ndi kuzokota miyala yoikika, ndi kozokota mtengo, kuchita ntchito zilizonse.