1
Matayo 5:15-16
Nyanja
NTNYBL2025
Wandhu saakweleza nyali ni kuikupika kwa debe. Nambho iyikidwa pamwamba poikila nyali kuti imulikile wandhu wonjhe yao ali mnyumba. Chimwecho dangalila lanu liwale pamaso pa wandhu kuti apenye vichito vanu vabwino ni kwaakweza Atate wanu akumwamba.”
Porovnat
Zkoumat Matayo 5:15-16
2
Matayo 5:14
“Anyiimwe ni dangalila la jhiko! Ni ngati nyumba iyo yamangidwa pamwamba pa phili siukhoza kubisika.
Zkoumat Matayo 5:14
3
Matayo 5:8
“Ali ni mwawi yao ali ni mtima wabwino pakuti saamuone Mnungu.”
Zkoumat Matayo 5:8
4
Matayo 5:6
“Ali ni mwawi yao afuna kupunda kuchita ivo vimkwadilicha Mnungu ndande Mnungu siwatangatile kuchita chimwecho.”
Zkoumat Matayo 5:6
5
Matayo 5:44
Nambho ine nikukambilani akondeni adani wanu ni kwapembhela anyiyao akuvutichani anyiimwe
Zkoumat Matayo 5:44
6
Matayo 5:3
“Ali ni mwawi wajha ajhiwa kuti amfuna Mnungu pakuti ufumu wa kumwamba ni wao.”
Zkoumat Matayo 5:3
7
Matayo 5:9
“Ali ni mwawi wajha apeleka mtendele pakuti siatanidwe wana a Mnungu.”
Zkoumat Matayo 5:9
8
Matayo 5:4
“Ali ni mwawi yao ali ni chisoni pakuti siathilidwe mtima.”
Zkoumat Matayo 5:4
9
Matayo 5:10
“Ali ni mwayi anyiyao avutichidwa ndande ya kuchita yayo wafuna Mnungu Pakuti ufumu wa kumwamba ni wao!”
Zkoumat Matayo 5:10
10
Matayo 5:7
“Ali ni mwawi wajha alengela wina lisungu pakuti Mnungu siwalengele lisungu.”
Zkoumat Matayo 5:7
11
Matayo 5:11-12
“Muli ni mwawi wandhu yapo sakutukwaneni ni kukuvutichani ni kukunamizilani voipa ndande yanga. Kondwani ni lulutilani pakuti chikho chanu chachikulu chaikidwa kumwamba. Mchimwecho nde umo adaavuticha alosi akhale anyiimwe mkali wosabdwa.”
Zkoumat Matayo 5:11-12
12
Matayo 5:5
“Ali ni mwawi yao ajhichicha pakuti Mnungu siwapache jhiko likhale lao.”
Zkoumat Matayo 5:5
13
Matayo 5:13
“Anyiimwe ni mchele wa chinyope wa jhiko. Nambho mchele wa chinyopeo ngati wasukuluka sikomelechedwe ni chiyani? Ulibe njhito. Siutaidwe kubwalo nikupondedwa ni wandhu.”
Zkoumat Matayo 5:13
14
Matayo 5:48
Chimwecho khalani wokwanila ngati Tate wanu wa kumwamba umo wali okwanila.”
Zkoumat Matayo 5:48
15
Matayo 5:37
Ukakamba, ‘Yetu’ basi ikhale ‘Yetu.’ Ukakamba, ‘Notho’ basi ikhale ‘Notho.’ Chalichonjhe icho chipitilila nghani zimenezo chichoka kwa Woyesa.”
Zkoumat Matayo 5:37
16
Matayo 5:38-39
“Mwavela kuti idakambidwa, ‘Diso kwa diso ni jhino kwa jhino.’ Nambho ine nikukambilani, msadabwezela mbwezo kwa mundhu uyo wakuchitila voipa. Mundhu wakakubula mbama kuchakaya la kwene chinchijha mleke wakubule chakaya lakawili.
Zkoumat Matayo 5:38-39
17
Matayo 5:29-30
Ngati diso lako la kwene likakuchiticha kuti uchite chimo lizule ni kulitaya kutali. Mbasa kutaiza chiwalo chimojhi cha thupi lako kusiyana ni thupi lako lonjhe kutaidwa ku jehanamu ya moto. Ngati jhanja lako la kwene likuchiticha kuti uchite chimo lidule ni ukalitaye kutali ni iwe. Mbasa kutaiza chiwalo chimojhi cha thupi lako kusiyana ni thupi lako lonjhe kutaidwa ku jehanamu ya moto.”
Zkoumat Matayo 5:29-30
Domů
Bible
Plány
Videa