1
Matayo 3:8
Nyanja
NTNYBL2025
Mchite vichito vijha vilangiza kuti mwayasiya machimo yanu.
Porovnat
Zkoumat Matayo 3:8
2
Matayo 3:17
Mwachizulumukila mvekelo kuchokela kumwamba udaveka, “Uyu nde Mwana wanga wokondedwa uyo nikondwela nayo.”
Zkoumat Matayo 3:17
3
Matayo 3:16
Pampajha, Yesu yapo wadamaliza kubatizidwa wadachuuka mmajhi. Kumwamba kudamasuka ni wadaona Mzimu wa Mnungu niuchika ngati nghunda ni kutula pamwamba pake.
Zkoumat Matayo 3:16
4
Matayo 3:11
Ine nikubatizani kwa majhi kulangiza kuti mwayasiya machimo yanu. Nambho uyo wakujha mmbuyo mwanga wali ni mbhamvu kupitilila ine. Ine sinifunika kutenga vingwe va malapasi yake. Iye siwakubatizeni kwa Mzimu Woyela ni moto.
Zkoumat Matayo 3:11
5
Matayo 3:10
Basi nghwangwa yathoikidwa kudula mizo. Chimwecho mtengo uliwonjhe uwo suubala vipacho vabwino suudulidwe ni kutayidwa pamoto.
Zkoumat Matayo 3:10
6
Matayo 3:3
Uyu nde Yohana yujha nghani zake zidakambidwa ni mlosi Isaya kuti, “Mundhu watana ku phululu, ‘Akonjeleni Ambuye njila yao tambasulani njila yake!’”
Zkoumat Matayo 3:3
Domů
Bible
Plány
Videa