1
MARKO 5:34
Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014
BLPB2014
Ndipo anati kwa iye, Mwana wamkaziwe, chikhulupiriro chako chakupulumutsa; muka mumtendere, nukhale wochira chivutiko chako.
Porovnat
Zkoumat MARKO 5:34
2
MARKO 5:25-26
Ndipo munthu wamkazi amene anali ndi nthenda yachidwalire zaka khumi ndi ziwiri, ndipo anamva zowawa zambiri ndi asing'anga ambiri, nalipira zonse anali nazo osachira pang'ono ponse, koma makamaka nthenda yake idakula
Zkoumat MARKO 5:25-26
3
MARKO 5:29
Ndipo pomwepo kasupe wa nthenda yake adaphwa; ndipo anazindikira m'thupi kuti anachiritsidwa chivutiko chake.
Zkoumat MARKO 5:29
4
MARKO 5:41
Ndipo anagwira dzanja lake la mwana, nanena kwa iye, Talita koumi , ndiko kunena posandulika, Buthu, ndinena ndi iwe, Uka.
Zkoumat MARKO 5:41
5
MARKO 5:35-36
M'mene iye ali chilankhulire, anafika a kunyumba ya mkulu wa sunagoge, nanena, kuti, Mwana wako wafa; uvutiranjinso Mphunzitsi? Koma Yesu wosasamala mau olankhulidwawo, ananena kwa mkulu wa sunagoge, Usaope, khulupirira kokha.
Zkoumat MARKO 5:35-36
6
MARKO 5:8-9
Pakuti ananena kwa iye, Tuluka iwe, mzimu wonyansa, kwa munthuyu. Ndipo anamfunsa, Dzina lako ndani? Ndipo ananena kwa Iye, Dzina langa ndine Legio; chifukwa tili ambiri.
Zkoumat MARKO 5:8-9
Domů
Bible
Plány
Videa