Luka 7:47-48

Luka 7:47-48 CCL

Tsono, ndikukuwuza iwe, machimo ake amene ndi ambiri akhululukidwa, monga chaonetsera chikondi chake chachikulu. Koma iye amene wakhululukidwa zochepa amakonda pangʼono.” Kenaka anati kwa mayiyo, “Machimo ako akhululukidwa.”

Imatge del verset per a Luka 7:47-48

Luka 7:47-48 - Tsono, ndikukuwuza iwe, machimo ake amene ndi ambiri akhululukidwa, monga chaonetsera chikondi chake chachikulu. Koma iye amene wakhululukidwa zochepa amakonda pangʼono.”
Kenaka anati kwa mayiyo, “Machimo ako akhululukidwa.”