Luka 5:5-6

Luka 5:5-6 CCL

Simoni anayankha kuti, “Ambuye, tagwira ntchito molimbika usiku wonse, koma sitinagwire kanthu. Koma pakuti mwatero, ndiponya makhoka.” Atachita izi, anagwira nsomba zambiri kotero kuti makhoka awo anayamba kungʼambika.