Logotip de YouVersion
La BíbliaPlansVídeos
Aconsegueix l'aplicació
Selector d'idiomes
Icona de cerca

Versets bíblics populars de Mateyu 22

1

Mateyu 22:37-39

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

CCL

Yesu anayankha kuti, “Uzikonda Yehova Mulungu wako ndi mtima wako wonse ndi moyo wako wonse ndi nzeru zako zonse. Ili ndi lamulo loyamba ndi loposa onse. Ndipo lachiwiri ndi lofanana nalo: ‘Konda mnansi wako monga iwe mwini.’

Compara

Explorar Mateyu 22:37-39

2

Mateyu 22:40

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

CCL

Malamulo onse ndi aneneri zakhazikika pa malamulo awiriwa.”

Compara

Explorar Mateyu 22:40

3

Mateyu 22:14

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

CCL

“Popeza oyitanidwa ndi ambiri koma osankhidwa ndi ochepa.”

Compara

Explorar Mateyu 22:14

4

Mateyu 22:30

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

CCL

Anthu akadzaukitsidwa, sadzakwatira kapena kukwatiwa; adzakhala ngati angelo kumwamba.

Compara

Explorar Mateyu 22:30

5

Mateyu 22:19-21

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

CCL

Onetseni ndalama imene mumapereka msonkho.” Iwo anabweretsa dinari, ndipo anawafunsa kuti, “Kodi chithunzi ichi ndi malemba awa ndi za ndani?” Iwo anayankha kuti, “Ndi za Kaisara.” Pamenepo anawawuza kuti, “Perekani kwa Kaisara zake za Kaisara, ndi kwa Mulungu zake za Mulungu.”

Compara

Explorar Mateyu 22:19-21

Plans de lectura i devocionals gratuïts relacionats amb Mateyu 22

Capítol anterior
Capítol següent
YouVersion

Animant-te i desafiant-te a buscar la intimitat amb Déu cada dia.

Ministeri

Sobre

Carreres

Fes-te voluntari

Blog

Premsa

Enllaços útils

Ajuda

Fer un donatiu

Versions de la Bíblia

Bíblia en àudio

Idiomes de la Bíblia

Verset del dia


Un Ministeri Digital de

Life.Church
Català

©2026 Life.Church / YouVersion

Política de privacitatCondicions d'ús
Programa de divulgació de vulnerabilitats
FacebookTwitterInstagramYouTubePinterest