Yohana 12:13
Yohana 12:13 NTNYBL2025
Ndiipo adatenga ndhawi za zing'onozing'ono za mitengo ya mitende, ni kupita kumlandila, adakweza mvekelo ni kukamba, “Uelekelo! Wapachidwe mwawi uyo wakujha kwa jhina la Ambuye. Wapachidwe mwawi Mfumu wa Izilaeli!”







