Maluko 12:41-42
Maluko 12:41-42 NTNYBL2025
Yesu wadakhala pafupi ni chombo choikila njhembe panyumba ya Mnungu. Wadaona wandhu umo amachochela njhembe. Wopata ambili adachocha ndalama zambili. Pamenepo wadajha maye mmojhi wafedwa ni mmunake uyo wadali wosauka, wadachocha senti ziwili.

