1
Marko 3:35
Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
CCL
Aliyense amene achita chifuniro cha Mulungu ndi mʼbale wanga ndi mlongo wanga ndi amayi anga.”
Yenzanisa
Ongorora {{vhesi}}
2
Marko 3:28-29
Ndikukuwuzani zoona kuti machimo onse ndi zamwano zonse za anthu zidzakhululukidwa, koma aliyense amene achitira mwano Mzimu Woyera sadzakhululukidwa pakuti wachita tchimo losatha.”
3
Marko 3:24-25
Ngati ufumu ugawanikana mwa iwo okha, ufumu umenewo sungakhalitse. Ngati nyumba igawanikana mwa iyo yokha, nyumba imeneyo singathe kuyima.
4
Marko 3:11
Nthawi iliyonse mizimu yoyipa ikamuona, imagwa pansi pamaso pake ndi kufuwula kuti, “Inu ndinu Mwana wa Mulungu!”