Eksodo 29:45-46

Eksodo 29:45-46 CCL

Ndidzakhala pakati pa Aisraeli ndikukhala Mulungu wawo. Adzadziwa kuti ine ndine Mulungu wawo amene ndinawatulutsa mʼdziko la Igupto kuti ndikhale pakati pawo. Ine ndine Yehova, Mulungu wawo.”