Eksodo 24:17-18

Eksodo 24:17-18 CCL

Ulemerero wa Yehova uja unkaoneka ngati malawi a moto pamwamba pa phirilo. Ndipo Mose analowa mʼmitambo nakwera phiri. Iye anakhala ku phiriko 40 usana ndi usiku.