1
Levitiko 23:3
Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
CCL
“ ‘Pa masiku asanu ndi limodzi muzigwira ntchito, koma tsiku lachisanu ndi chiwiri ndi Sabata lopuma, tsiku la msonkhano wopatulika. Kulikonse kumene inu mukukhala musamagwire ntchito iliyonse tsiku limeneli popeza ndi tsiku la Sabata la Yehova.
Porównaj
Przeglądaj Levitiko 23:3