Maluko 10
10
Talaka
Matayo 19:1-12; Luka 16:18
1Ndiipo Yesu wadachoka ku Kapelinaumu ni kupita ku mujhi wa Yudeya, ni kuyomboka mchinje Yolodani. Gulu la wandhu lidamchatanjho, niiiye wadaayaluza ngati umo idali kalidwe chake.
2Afalisayo akumojhi adamchata, ni adamfunjha kwa kumuyesa, “Bwanji, thauko lathu litilola wamuna kumsiya mkazake?” 3Yesu wadaafunjha, “Bwanji, Musa wadakulamulani chiyani?” 4Anyiiwo adamuyahga, “Musa wadaagiza wammuna wakhoza kulemba talaka ni kumsiya wamkazi.”
5Yesu wadaakambila, “Musa wadakulembelani lamulo limenelo ndande simuyaluzika. 6Nambho, kuyambila kuumbidwa kwa jhiko, Mnungu wadaumba wamuna ni wamkazi. 7Chimwecho, wamuna siwasiye atate wake ni amake ni kulunjana ni mkazake, 8ni anyiiwo awili sakhale thupi limojhi. Chipano anyiiwo osati awilinjho, nambho ni thupi limojhi. 9Chimwecho, icho wachilunjanicha Mnungu, mundhu siwadachisiyanicha.”
10Yapo adabwelanjho mnyumba, oyaluzidwa adamfunjha Yesu kuusu chindhu chimenecho cho siyana. 11Yesu wadaakambila, “Wammuna waliyonjhe uyo wamsiya wamkazi ni kukwata mwina, wamchitila chigololo mkazake. 12Chinchijha, wamkazi wakamsiya mmunake ni kupita kukwatiwa ni wammuna mwina, wamchitila chigololo mmunake.”
Yesu wapacha mwawi wana waang'onoang'ono
Matayo 19:13-15; Luka 18:15-17
13Wandhu wina adampelekela Yesu wana wang'onoang'ono waikile manja kuti wapache mwawi, nambho oyaluzidwa wake adaakaniza. 14Yesu yapo wadaona chimwecho, wadakwiya ni kwaakambila, “Asiyeni wana waang'onoang'ono ajhe kwanga, ni simdachelekeza, ndande wandhu ali ngati wana anyiiawa nde sialowe muufumu wa Mnungu. 15Zenedi nikukambilani, mundhu waliyonjhe uyo siwaulandila Ufumu wa Mnungu ngati wana wang'onoang'ono umo aulandilila, siwalowelatu muufumu wa Mnungu.” 16Ndiipo wadakhumbatila wana achameneo, ni kwaikila manja, ni kwaapacha mwawi.
Mundhu wopata
Luka 18:18-30
17Yesu yapo wamachoka, mundhu mmojhi wadamthamangila ni kumgwadila, wadamfunjha, “Oyaluza wabwino, nichite chiyani niupate umoyo wa muyaya?” 18Yesu wadamfunjha “Ndande yanji unitana wabwino? Palibe mundhu wali wabwino, nambho Mnungu yokha. 19Ulijhiwa thauko la musa, ‘Siudapha, siudachita chigololo, siudaba, siudachocha umboni wa unami, siudanyenga, walemekeze amako ni atate wako.’”
20Mundhu mmeneyo wadayangha, “Oyaluza, thauko limenelo lonjhe nazichata kuyambila kuubwana wanga.”
21Yesu wadampenya ni wadamkonda, ni wadamkambila, “Wachepekeledwa ni chindhu chimojhi, pita ukaguliche kila chindhu ulinacho, ni ndalama izo siupate waapache wosauka, niiwe siukhale ni wopata kumwamba, ndiipo majha unichate.” 22Mundhu mmeneyo yapo wadavela chimwecho, wadadandaula mumtima, wadachoka uku wali ni chisoni, pakuti wadali ni chuma chambili.
23Yesu wadapenya konjhekonjhe, wadaakambila oyaluzidwa wake, “Siikhale kulimba kwa mundhu wopata kulowa mu Ufumu wa Mnungu!” 24Oyaluzidwa wake adazizwa kupunda yapo adavela nghani zimenezo. Yesu wadaakambilanjho, “Anyabwenjilanga, ilimba kupunda kwa mundhu, kulowa mu Ufumu wa Mnungu. 25Siikhale lahisi kwa nyama iyo itanidwa ngamila kulowa pa ndhoolo ya sindano, nambho osati wopata kulowa mu Ufumu wa Mnungu.” 26Oyaluzidwa wake adazizwa kupunda, adafunjhana, “Niyani basi uyo siwakhoze kuomboledwa?” 27Yesu wadaapenyechecha ni kwaakambila, “Kwa mundhu siikhozekana, nambho kwa Mnungu ikhozekana, pakuti kila kandhu kwa Mnungu chikhozekana.”
28Petulo wadamkambila, “Ife tasiya kilakandhu takuchata iwe.” 29Yesu wadakamba, “Zenedi nikukambiulani, kila mundhu uyo waisiya wandhu amnyumba yake, kapina mbale wake, kapina mlongo wake, kapina maye wake, kapina atate wake, kapina wana wake kapina minda yake ndande yaine ni ndande ya Uthenga Wabwino, 30siwalandile vindhu vochuluka pa ndhawi ya saino. Siwalandile nyumba, abale, alongo, maye, wana ni minda ni mavuto, ni masiku yayo yakujha siwalandile umoyo wa muyaya. 31Nambho, yawo achogolela siakhale kumbuyo, ni akumbuyo siachogolele.”
Yesu wakamba mala ya katatu nghani za nyifa yake ni kuhyuka
Matayo 20:17-19; Luka 18:31-34
32Yesu ni oyaluzidwa wake, adali mnjila amakwela kupita kumujhi wa Yelusalulemu, ni Yesu wadatowachogolela. Oyaluzidwa wake adazizwa, ni wandhu wonjhe yawo amamchata adaopa. Yesu wadaatenga oyaluzidwa wake khumi ni awilil kumbhepete, wadayamba kwakambila yajha siyampheze, 33Yesu wadaakambila, “Vechelani, tipita ku Yelusalemu, nikumeneko Ine Mwana wa Mundhu siniikidwe mmanja mwa akuluakulu wa ajhukulu ni oyaluza thauko, ni anyiiwo siamlamule waphedwe ni kupachidwa kwa wandhu yawo osati Ayahudi. 34Ni anyiiwo sianipepule, ni kunilavulila malovu, siambule mikwapulo ni kumpha. Nambho siku la katatu siwahyuke.”
Yakobo ni Yohana ampembha Yesu ukulu
Matayo 20:20-28
35Ndiipo Yohana ni Yakobo, wana wa Zebadayo, adamchata Yesu nikumkambila, “Oyaluza, kuli chindhu tifuna mtichitile.” 36Yesu wadaafunjha, “Mfuna nikuchitileni chiyani?” 37Adamuyangha, “Yapo simkhale pampando wanu wachifumu pa ulemelelo wanu, tipembha mmojhi wakhale bendeka lanu la kumanjele, ni mwina bendeka lanu la kwene.” 38Yesu wadaayangha, “Simjhiwa icho mpembha! Bwanji, simkhoze kuvutika ngati umo sinivutikile ine, kapina kuphedwa ngati umo siniphedwele ine?” 39Adamuyangha, “Tikhoza.” Yesu wadaakambila, “Zenedi, simvutike ngati umo sinivutikile ine, ni simufe ngati umo sinifele ine. 40Nambho ni yani uyo siwakhale kwene ni kumanjele kwanga, osati njhito yaine, ni malo yameneyo siakhale yawo asanghidwa ni Mnungu.”
41Wajha oyaluzidwa wina khumi yapo adavela chijha adapembha Yakobo ni Yohana, adaakwiila. 42Chimwecho, Yesu wadaatana, wadaakambila, “Mjhiwa kuti anyiwajha aoneka kuti ni alamuli a wandhu anyiyawo osati Ayahudi, walamula wandhu kwa mbhavu, kuti wandhu wao avele. 43Nambho kwa anyiimwe siidakhala chimwecho, mundhu waliyonjhe uyo wafuna wakhale wamkulu, ifunika wakhale mbowa wa wonjhe. 44Mundhu waliyonjhe uyo wafuna kukhala wamkulu, ifunika wajhatumikila wonjhe. 45Ata, ine Mwana wa Mundhu sinidajhe kutumikilidwa, nambho kutumukila, ni kuchocha umoyo wanga kwa kwaombola wandhu ambili.”
Yesu wamlamicha mudhu wosapenye Batimayo
Matayo 20:29-34; Luka 18:35-43
46Ndiipo, adafika ku Yeliko. Yesu ni oyaluzidwa wake pamojhi ni gulu lalikulu la wandhu, adampheza mundhu mmojhi wosapenya, uyo wamatanidwa Batimayo, mwana wa Timayo, wakhala pambhepete pa njila niwapembha pembha vindhu. 47Batimayo yapo wadavela kuti Yesu wa ku Nazaleti wamapita pamalo yameneyo, wadakweza mvekelo wake, niwakamba, “Imwe a Yesu, Mwana wa Daudi nilengeleni lisungu!” 48Wandhu ambili adamnyindila, adamkambila wakhale chete, nambho iye wadapunda kukweza mvekelo, “Imwe Mwana wa Daudi, nilengeleni lisungu”
49Yesu wadaima, ni kukamba “Mkambileni wajhe.” Ndiipo adamtana, adamkambila, “Jhipache mtima, ima watokutana.” 50Niiye wadataya kutali njhalu yake, wadalumbha ni kumpitila Yesu.
51Yesu wadamfunjha, “Ufuna nikuchitile chiyani?” Sapenya yujha wadamuyangha, “Oyaluza, nipemhba nipenye.”
52Yesu wadamkambila, “Pita, kukhulupilila kwako kwakulamicha.” Pampajha, yujha sapenya wadakhoza kupenya, ndiipo wadamchata Yesu mnjila.
നിലവിൽ തിരഞ്ഞെടുത്തിരിക്കുന്നു:
Maluko 10: NTNYBL2025
ഹൈലൈറ്റ് ചെയ്യുക
പങ്ക് വെക്കു
പകർത്തുക

നിങ്ങളുടെ എല്ലാ ഉപകരണങ്ങളിലും ഹൈലൈറ്റുകൾ സംരക്ഷിക്കാൻ ആഗ്രഹിക്കുന്നുണ്ടോ? സൈൻ അപ്പ് ചെയ്യുക അല്ലെങ്കിൽ സൈൻ ഇൻ ചെയ്യുക
The New Testament in Nyanja @The Word for The World International and Nyanja Language translation, 2025. All rights reserved.

: