Maluko 11
11
Yesu walowa ku Yelusalemu kwa chikondwelo
Matayo 21:1-11; Luka 19:28-40; Yohana 12:12-19
1Yesu ni oyaluzidwa wake yapo adafika ku Yelusalemu, ku vijhijhi va Besifage ni ku Besania, pafupi ni phili la Mizeituni, wadaatuma oyaluzidwa wake awili amchogolele. 2Wadaakambila, “Pitani kukijhijhi chili pachogolo panu. Yapo simmalowe mmenemo, simpheze mwana wa phunda, uyo siwadatumike ni mundhu waliyonjhe. Mmasuleni ni mjhenayo. 3Ngati mundhu wakakufunjhani ndande yanji mummasula, myangheni kuti Ambuye atomfuna ni sambweze chipanoyapa.”
4Anyiwajha oyaluzidwa adachoka, ni adampheza mwana wa phunda wamangidwa pafupi ni pakhomo la nyumba, mbhepete mwa njila. Yapo amammasula, 5wandhu wina yawo adali pamenepo, adaafunjha, “Mchita chiyani? Ndande yanji mummasula mwana wa phundayo?” 6Oyaluzidwa wajha adayangha ngati umo Yesu wadaakambila, ni wandhu achamenewo adaasiya apitenayo. 7Adampeleka yujha mwana phunda kwa Yesu. Adayala njhalu zao pamsana pa yujha mwana punda, ni Yesu wadakwela pamsana ni kukhala. 8Wandhu ambili adayala njhalu zao mnjila, ni wina adadula ndhawi zazing'onozing'ono za mitengo adaziyala mnjila ndande ya kumlemekeza Yesu. 9Wandhu wonjhe adamchogolela ni anyiwajha amamchata mmbuyo, adakweza mvekelo niakamba, “Mtamandeni Mnungu! Wapachidwe mwawi uyo wakujha kwa jhina la Ambuye! 10Mnungu waupache mwawi Ufumu uwo ukujha wa atate wathu mfumu Daudi. Watamandidwe Mnungu uyo wali kumwamba kupunda.”
11Yesu wadalowa kumujhi wa ku Yelusalemu ni kupita mbaka kunyumba ya Mnungu, wadapenyechecha kila chindhu. Nambho, ndande jhuwa lidabila, wadapita ku Besania pamojhi ni anyiwajha oyaluzidwa wake khumi ni awili.
Yesu wauleswa mtengo wa mtini
Matayo 21:18-19
12Umawa wake yapo amachoka ku Besania kupita ku Yelusalemu, Yesu wadali ni njala. 13Wadauona mtengo wa mtini kwa patali, uwo udali ni machamba yambili. Wadauchata kuti wapenye ngati wakhoza kupheza chipacho chalichonjhe. Nambho yapo wadauwandikila, wadauona ulibe chipacho chalichonjhe, nambho udali ni machamba yokha, pakuti nyengo ya yobala vipacho idali ikali. 14Yesu wadaukambila ujha mtengo wa mtini, “Kuyambila lelo mbaka muyaya, siubalanjho.” Ni oyaluzidwa wake adamvela yapo wadakamba chimwecho.
Yesu wafika panyumba ya Mnungu
Matayo 21:12-17; Luka 19:45-48; Yohana 2:13-22
15Ndiipo, adafika ku Yelusalemu, Yesu wadafika panyumba ya Mnungu, wadayamba kwatopola kubwalo wandhu yawo amagulicha ni kugula vindhu pamenepo. Wadagadabula meza zaanyiwajha amang'anamucha ndalama, ni mipando ya anyiwajha amagulicha nghunda. 16Nisiwadamlole mundhu waliyonjhe watenge chindhu chalichonjhe kuchoka panyumba ya Mnungu. 17Ndiipo wadaayaluza, “Bwanji, siidalembedwe mmalemba yoyela, kuti, ‘Nyumba yanga siikhale malo ya mapembhelo ya wandhu amaiko yonjhe?’ Nambho anyiimwe mwaichita kukhala mbhanga ya anghungu.”
18Waakuluakulu wa ajhukulu ni oyaluza thauko yapo adavela yameneyo, adayamba kufunafuna njila ya kumpha Yesu. Nambho amamuopa, ndande ya gulu la wandhu wonjhe lidazizwa ni mayaluzo yake. 19Yapo ujhulo udajha, Yesu ni ochatila wake adachoka mujhi wa ku Yelusalemu.
Yaluzo la mtengo wa mtini uwo udauma
Matayo 21:20-22
20Umawamawa, yapo amapita, adauwona ujha mtengo wa mtini wauma wonjhe. 21Petulo wadakumbukila icho wadakamba Yesu, wadamkambila, “Oyaluza penyani, ujha mtengo wamtini mdauleswa, wauma”
22Yesu wadamkambila, “Mkhulupilileni Mnungu. 23Nikukambilani uzene, mundhu waliyonjhe wakalikambila phili ili kuti lipite likajivyale mnyanja ya mchele, popande kukhaikila mumtima mwake, nambho wakakhulupilia kuti chindhu icho wachikamba sichichokele, ni Mnungu siwamchitile. 24Chipano nikukambilani, yapo msali ni kupembha chindhu, khulupililani kuti mwachilandila, nianyiimwe simchipate. 25Ni yapo mpembhela, mlekelelane, kila mundhu wamlekelele mnjake uyo wamlakwila, ni Atate wanu ali kumwamba siakulekeleleni anyiimwe volakwa vanu. 26Nambho ngati simwalekelela wina, ni Atate wanu ali kumwamba siakulekelelani anyiimwe volakwa vanu.”
Nghani kuusu ulamulilo wa Yesu
Matayo 21:23-27; Luka 20:1-8
27Ndiipo, adafikanjho ku Yelusalemu. Yesu yapo wamaenda panyumba ya Mnungu, waakulu akulu wa ajhukulu, ni oyaluza thauko ni azee adamchata, 28adamfunjha, “Bwanji, uchita yaya kwa ulamulilo wa yani? Yani wakupacha ulamulilo wochita vindhu ivi?”
29Yesu wadaayangha, “Nikufunjheni funjho limojhi, mkaniyangha, ni ine sinikukambileni nichita yaya kwa ulamulilo wa yani. 30Nikambileni, ulamulilo wo batiza wa Yohana udachokela kuti, kwa Mnungu kapina kwa wandhu?”
31Adayamba kukambilana, “Tikakamba, ‘Ulamulilo wake wobatiza wachoka kwa Mnungu,’ hiwatifunjhe, ‘Ndande yanji sidamkhulupilile.’ 32Nambho tikakamba kuti, ‘Ulamulilo wake Wachoka kwa wandhu,’ wandhuwo saipile.” Amaopa gulu la wandhu, pakuti wandhu wonjhe adajhiwa kuti Yohana wadali mlosi. 33Basi adayangha, “Ife sitijhiwa.” Naye Yesu wadaakambila “Niine sinikukambilani kuti nichita yaya kwa ulamulilo wanji.”
നിലവിൽ തിരഞ്ഞെടുത്തിരിക്കുന്നു:
Maluko 11: NTNYBL2025
ഹൈലൈറ്റ് ചെയ്യുക
പങ്ക് വെക്കു
പകർത്തുക

നിങ്ങളുടെ എല്ലാ ഉപകരണങ്ങളിലും ഹൈലൈറ്റുകൾ സംരക്ഷിക്കാൻ ആഗ്രഹിക്കുന്നുണ്ടോ? സൈൻ അപ്പ് ചെയ്യുക അല്ലെങ്കിൽ സൈൻ ഇൻ ചെയ്യുക
The New Testament in Nyanja @The Word for The World International and Nyanja Language translation, 2025. All rights reserved.

: