Logo YouVersion
BibPlan yoVideyo
Pran aplikasyon an
Seleksyone Lang
Chache Icon

Vèsè popilè nan Bib la ki soti nan MACHITIDWE A ATUMWI 26

1

MACHITIDWE A ATUMWI 26:17-18

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

BLPB2014

ndi kukulanditsa kwa anthu, ndi kwa amitundu, amene Ine ndikutuma kwa iwo, kukawatsegulira maso ao, kuti atembenuke kuchokera kumdima, kulinga kukuunika, ndi kuchokera ulamuliro wa Satana kulinga kwa Mulungu, kuti alandire iwo chikhululukiro cha machimo, ndi cholowa mwa iwo akuyeretsedwa ndi chikhulupiriro cha mwa Ine.

Konpare

Eksplore MACHITIDWE A ATUMWI 26:17-18

2

MACHITIDWE A ATUMWI 26:16

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

BLPB2014

Komatu uka, imirira pa mapazi ako; pakuti chifukwa cha ichi ndinaonekera kwa iwe, kukuika iwe ukhale mtumiki ndi mboni ya izi wandionamo Ine, ndiponso ya izi ndidzakuonekeramo iwe

Konpare

Eksplore MACHITIDWE A ATUMWI 26:16

3

MACHITIDWE A ATUMWI 26:15

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

BLPB2014

Ndipo ndinati, Ndinu yani Mbuye? Ndipo Ambuye anati, Ine ndine Yesu amene iwe umlondalonda.

Konpare

Eksplore MACHITIDWE A ATUMWI 26:15

4

MACHITIDWE A ATUMWI 26:28

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

BLPB2014

Ndipo Agripa anati kwa Paulo, Ndi kundikopa pang'ono ufuna kundiyesera mkhristu.

Konpare

Eksplore MACHITIDWE A ATUMWI 26:28

Plan lekti ak devosyon gratis yo ki gen rapò ak MACHITIDWE A ATUMWI 26

Chapit Avan yo
Chapit suivan
YouVersion

Ankouraje ak defi pou w chèche entimite ak Bondye chak jou.

Ministè

Apwopo

Karyè yo

Volontè

Blòg

Peze

Lyen itil yo

Ed

Fè yon don

Vèsyon Bib yo

Odyo Bib yo

Diferan Lang yo nan Bib la

Vèsè Jodi a


Yon Ministè Digital nan

Life.Church
English (US)

©2025 Life.Church / YouVersion

Politik PriveTèm yo
Pwogram Divilgasyon Vilnerabilite
FacebookTwitterInstagramYouTubePinterest

Akèy

Bib

Plan yo

Videyo