1
MACHITIDWE A ATUMWI 24:16
Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014
BLPB2014
M'menemonso ndidziyesera ndekha ndikhale nacho nthawi zonse chikumbu mtima chosanditsutsa cha kwa Mulungu ndi kwa anthu.
Konpare
Eksplore MACHITIDWE A ATUMWI 24:16
2
MACHITIDWE A ATUMWI 24:25
Ndipo m'mene anamfotokozera za chilungamo, ndi chidziletso, ndi chiweruziro chilinkudza, Felikisi anagwidwa ndi mantha, nayankha, Pita tsopano; ndipo ndikaona nthawi, ndidzakuitana iwe.
Eksplore MACHITIDWE A ATUMWI 24:25
Akèy
Bib
Plan yo
Videyo