Logo de YouVersion
Icono de búsqueda

AROMA 5:3-4

AROMA 5:3-4 BLPB2014

Ndipo si chotero chokha, komanso tikondwera m'zisautso; podziwa ife kuti chisautso chichita chipiriro; ndi chipiriro chichita chizolowezi; ndi chizolowezi chichita chiyembekezo