AEFESO 5:1-2
AEFESO 5:1-2 BLPB2014
Chifukwa chake khalani akutsanza a Mulungu, monga ana okondedwa; ndipo yendani m'chikondi monganso Khristu anakukondani inu, nadzipereka yekha m'malo mwathu, chopereka ndi nsembe kwa Mulungu, ikhale fungo lonunkhira bwino.












