Logo de YouVersion
Icono de búsqueda

MACHITIDWE A ATUMWI 9:17-18

MACHITIDWE A ATUMWI 9:17-18 BLPB2014

Ndipo anachoka Ananiya, nalowa m'nyumbayo; ndipo anaika manja ake pa iye, nati, Saulo, mbale, Ambuye wandituma ine, ndiye Yesu amene anakuonekerani pa njira wadzerayo, kuti upenyenso, ndi kudzazidwa ndi Mzimu Woyera. Ndipo pomwepo padagwa kuchoka m'maso mwake ngati mamba, ndipo anapenyanso; ndipo ananyamuka nabatizidwa

Planes de lectura y devocionales gratis relacionados con MACHITIDWE A ATUMWI 9:17-18