Yesu wadaendekela kuyaluza, “Yapo mmanga simdalingana ni agunghuli yawo achita nghope zao zionekane kuti zili ni chisoni kuti aoneke amanga. Nikukambilani uzene achamenewo atholandila chikho chao. Yapo umanga usambe kumaso kwako ni unyeke mafuta mmutu mwako, kuti wandhu siwadajhiwa kuti wamanga kudya nambho ajhiwe Atate wakope yao saonekana. Nawo Atate wako yao aona yayo yabisika sakupache chikho.”