1
Matayo 18:20
Nyanja
NTNYBL2025
Pakuti yapo asonghana wandhu awili kapina atatu kwa jhina langa, ine nili pamojhi nao.”
Comparar
Explorar Matayo 18:20
2
Matayo 18:19
“Zene nikukambilani, awili pakati panu akavomelezana pajhiko la panjhi kuusu chilichonjhe icho afuna kupembha, Atate wanga a kumwamba siakuchitileni.
Explorar Matayo 18:19
3
Matayo 18:2-3
Yesu wadamtana mwana wamng'ono ni kumwimika pakati pao, Ndiipo wadaakambila, “Zene nikukambilani, ngati simng'anamuka ni kulingana ni wana waang'onoang'ono, simulowa mu Ufumu wa kumwamba.
Explorar Matayo 18:2-3
4
Matayo 18:4
Waliyonjhe uyo wajhichepecha ngati mwana uyu, nde uyo siwakhale wamkulu mu Ufumu wa kumwamba.
Explorar Matayo 18:4
5
Matayo 18:5
Uyo wamlandila mwana wamng'ono ngati uyu kwa jhina langa, wanilandila ine.”
Explorar Matayo 18:5
6
Matayo 18:18
“Zene ikukambilani, yayo simuyamange pajhiko la panjhi chinchijha siyamangidwe kumwamba, ni icho simuchimasule pajhiko la panjhi chinchijha sichimasulidwe kumwamba.
Explorar Matayo 18:18
7
Matayo 18:35
Yesu wadamaliza pokamba, “Umu ndeumo Atate wanga akumwamba siakuchiteni ngati simwaalekelela achanjanu volakwa vao.”
Explorar Matayo 18:35
8
Matayo 18:6
“Ngati mundhu waliyonjhe uyo wamchiticha mmojhi wa wana yawa kuchita chimo, idakakhala mbasa kwa mundhu mmeneyo wamangidwe mbhelo mkhosi mwake ni kubizidwa kuchilundu.
Explorar Matayo 18:6
9
Matayo 18:12
“Muona bwanji ngati mundhu wali ni mbelele miya mojha, ikasowa imojhi, wachita bwanji? Wazisia zijha tisini ni tisa mkhola, nikupita kuifunafuna ijha yasowa.
Explorar Matayo 18:12
Inicio
Biblia
Planes
Vídeos