1
MACHITIDWE A ATUMWI 24:16
Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014
BLPB2014
M'menemonso ndidziyesera ndekha ndikhale nacho nthawi zonse chikumbu mtima chosanditsutsa cha kwa Mulungu ndi kwa anthu.
Comparar
Explorar MACHITIDWE A ATUMWI 24:16
2
MACHITIDWE A ATUMWI 24:25
Ndipo m'mene anamfotokozera za chilungamo, ndi chidziletso, ndi chiweruziro chilinkudza, Felikisi anagwidwa ndi mantha, nayankha, Pita tsopano; ndipo ndikaona nthawi, ndidzakuitana iwe.
Explorar MACHITIDWE A ATUMWI 24:25
Inicio
Biblia
Planes
Vídeos