1
MACHITIDWE A ATUMWI 20:35
Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014
BLPB2014
M'zinthu zonse ndinakupatsani chitsanzo, chakuti pogwiritsa ntchito, kotero muyenera kuthandiza ofooka ndi kukumbuka mau a Ambuye Yesu, kuti anati yekha, Kupatsa kutidalitsa koposa kulandira.
Comparar
Explorar MACHITIDWE A ATUMWI 20:35
2
MACHITIDWE A ATUMWI 20:24
Komatu sindiuyesa kanthu moyo wanga, kuti uli wa mtengo wake kwa ine ndekha; kotero kuti ndikatsirize njira yanga, ndi utumiki ndinaulandira kwa Ambuye Yesu, kuchitira umboni Uthenga Wabwino wa chisomo cha Mulungu.
Explorar MACHITIDWE A ATUMWI 20:24
3
MACHITIDWE A ATUMWI 20:28
Tadzichenjerani nokha, ndi gulu lonse, pamenepo Mzimu Woyera anakuikani oyang'anira, kuti muwete Mpingo wa Mulungu, umene anaugula ndi mwazi wa Iye yekha.
Explorar MACHITIDWE A ATUMWI 20:28
4
MACHITIDWE A ATUMWI 20:32
Ndipo tsopano ndikuikizani kwa Mulungu, ndi kwa mau a chisomo chake, chimene chili ndi mphamvu yakumangirira ndi kupatsa inu cholowa mwa onse oyeretsedwa.
Explorar MACHITIDWE A ATUMWI 20:32
Inicio
Biblia
Planes
Vídeos