1
MACHITIDWE A ATUMWI 13:2-3
Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014
BLPB2014
Ndipo pa kutumikira Ambuye iwowa, ndi kusala chakudya, Mzimu Woyera anati, Mundipatulire Ine Barnabasi ndi Saulo ku ntchito imene ndinawaitanirako. Pamenepo, m'mene adasala chakudya ndi kupemphera ndi kuika manja pa iwo, anawatumiza amuke.
Comparar
Explorar MACHITIDWE A ATUMWI 13:2-3
2
MACHITIDWE A ATUMWI 13:39
ndipo mwa Iye yense wokhulupirira ayesedwa wolungama kumchotsera zonse zimene simunangathe kudzichotsera poyesedwa wolungama ndi chilamulo cha Mose.
Explorar MACHITIDWE A ATUMWI 13:39
3
MACHITIDWE A ATUMWI 13:47
Pakuti kotero anatilamula Ambuye ndi kuti, Ndakuika iwe kuunika kwa amitundu, kuti udzakhala iwe chipulumutso kufikira malekezero a dziko.
Explorar MACHITIDWE A ATUMWI 13:47
Inicio
Biblia
Planes
Vídeos