1
Maluko 1:35
Nyanja
NTNYBL2025
Umawamawa siku lidachatila, Yesu wadapita kubwalo kwa mujhi, pamalo yapo padalibe wandhu, kumeneko wadampembha Mnungu.
Ṣe Àfiwé
Ṣàwárí Maluko 1:35
2
Maluko 1:15
Wadakamba, “Nyengo ya Mnungu yakwana yolamulila wandhu. Lapani ni kukhulupilila Uthenga Wabwino.”
Ṣàwárí Maluko 1:15
3
Maluko 1:10-11
Yesu yapo wadachuuka mmajhi, pamwepo wadaona kumwamba kwamasulidwa, ni Mzimu Woyela udamchikila ngati nghunda. Mvekelo wa Mnungu udaveka kuchokela kumwamba, niukamba, “Iwe nde mwana wanga uyo nikukonda, nikondelechedwa ni iwe.”
Ṣàwárí Maluko 1:10-11
4
Maluko 1:8
Ine nikubatizani kwa majhi, nambho iye siwakubatizeni kwa Mzimu Woyela.”
Ṣàwárí Maluko 1:8
5
Maluko 1:17-18
Yesu wadaakambila, “Nichateni, nane sinikuyaluzeni mukhale owapeleka wandhu kwa ine, ngati umo mmavuwila njhomba.” Pampajha adavisia vilepa vao nikumchata.
Ṣàwárí Maluko 1:17-18
6
Maluko 1:22
Wandhu yawo adamvela mayaluzo yake, adazizwa ndande siwamayaluze ngati umo amayaluzila oyaluza athauko la Musa, nambho iye wamayaluza ngati mundhu wa ulamulilo.
Ṣàwárí Maluko 1:22
Ilé
Bíbélì
Àwon ètò
Àwon Fídíò