Logo ya YouVersion
Elilingi ya Boluki

Matayo 24:9-11

Matayo 24:9-11 NTNYBL2025

“Ndiipo sakugwileni kuti mvutichidwe ni kuphedwa. Wandhu a maiko yonjhe siyakuipileni ndande anyiimwe ni oyaluzidwa wanga. Nyengo imeneyo, wandhu ambili yawo anikhulupilila siasiye kunikhulupilila, ni kung'anamukana ni kuipilana. Siachokele alosi ambili amthila, ni anyiiwo siwanyenge wandhu ambili.