AROMA 11:5-6

AROMA 11:5-6 BLPB2014

Choteronso nthawi yatsopano chilipo chotsalira monga mwa kusankha kwa chisomo. Koma ngati kuli ndi chisomo, sikulinso ndi ntchito ai; ndipo pakapanda kutero, chisomo sichikhalanso chisomo.