MACHITIDWE A ATUMWI 20:28

MACHITIDWE A ATUMWI 20:28 BLPB2014

Tadzichenjerani nokha, ndi gulu lonse, pamenepo Mzimu Woyera anakuikani oyang'anira, kuti muwete Mpingo wa Mulungu, umene anaugula ndi mwazi wa Iye yekha.