MACHITIDWE A ATUMWI 17:24

MACHITIDWE A ATUMWI 17:24 BLPB2014

Mulungu amene analenga dziko lapansi ndi zonse zili momwemo, Iyeyo, ndiye mwini kumwamba ndi dziko lapansi, sakhala m'nyumba za kachisi zomangidwa ndi manja