1
GENESIS 30:22
Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014
BLPB2014
Ndipo Mulungu anakumbukira Rakele, ndipo Mulungu anamvera iye, natsegula m'mimba mwake.
Konpare
Eksplore GENESIS 30:22
2
GENESIS 30:24
namutcha dzina lake Yosefe; ndipo anati, Yehova anandionjezera ine mwana wamwamuna wina.
Eksplore GENESIS 30:24
3
GENESIS 30:23
Ndipo anatenga pakati, nabala mwana wamwamuna, nati, Mulungu wachotsa manyazi anga
Eksplore GENESIS 30:23
Akèy
Bib
Plan yo
Videyo