לוגו של YouVersion
כתבי הקודשתכניותקטעי וידאו
הורד את האפליקציה
בורר שפה
סמל חיפוש

פסוקים פופולריים מ- Gen. 12

1

Gen. 12:2-3

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

BLY-DC

Ndidzakusandutsa kholo la mtundu waukulu, ndipo ndidzakudalitsa ndi kukusandutsa wotchuka, kotero kuti udzakhala ngati dalitso kwa anthu ena. “Ndidzadalitsa onse okudalitsa iwe, koma ndidzatemberera aliyense wokutemberera. Mitundu yonse ya pa dziko lapansi idzapeza madalitso kudzera mwa iwe.”

השווה

חקרו Gen. 12:2-3

2

Gen. 12:1

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

BLY-DC

Tsiku lina Chauta adauza Abramu kuti, “Choka kudziko kwako kuno. Usiye abale ako ndi banja la bambo wako, ndipo upite ku dziko limene nditi ndikusonyeze.

השווה

חקרו Gen. 12:1

3

Gen. 12:4

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

BLY-DC

Abramu anali wa zaka 75 pamene ankachoka ku Harani monga Chauta adaamlamulira, ndipo Loti adapita naye limodzi.

השווה

חקרו Gen. 12:4

4

Gen. 12:7

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

BLY-DC

Chauta adaonekera Abramu namuuza kuti, “Dziko limeneli ndidzapatsa zidzukulu zako.” Choncho pa malo amenewo Abramu adamanga guwa, kumangira Chauta amene adaamuwonekera.

השווה

חקרו Gen. 12:7

לפרק הקודם
לפרק הבא
YouVersion

מעודד ומאתגר אתכם לקשר הדוק עם אלוהים בכל יום.

מִשׂרָד

אודות

קריירה

התנדב

בלוג

לחץ

קישורים שימושיים

עזרה

תרום

גרסאות הכתובים

אודיו הכתובים

שפות התנ"ך

הפסוק של היום


משרד דיגיטלי של

Life.Church
English (US)

©2025 Life.Church / YouVersion

מדיניות פרטיותתנאים
תוכנית לגילוי חולשות אחראי
פייסבוקטוויטראינטגרםיוטיובפינטרסט

בית

כתבי הקודש

תכניות

קטעי וידאו