Yesu wadaendekela kukamba, “Mkhale maso msadachita vindhu vabwino pamaso pa wandhu kuti akuoneni. Ngati mchita chimwecho, Atate wanu ali kumwamba saakupachani chikho chalichonjhe.”
Matayo 6:1
Ilé
Bíbélì
Àwon ètò
Àwon Fídíò