Mufananidzo weYouVersion
Mucherechedzo Wekutsvaka

Zekariya 1:17

Zekariya 1:17 CCL

“Lengezanso kuti, Yehova Wamphamvuzonse akuti, ‘Mizinda yanga idzakhalanso ndi zokoma zosefukira ndipo Yehova adzatonthoza Ziyoni ndi kusankhanso Yerusalemu.’ ”