EKSODO 25:8-9
EKSODO 25:8-9 BLPB2014
Ndipo andimangire malo opatulika; kuti ndikhale pakati pao. Monga mwa zonse Ine ndilikuonetsa iwe, chifaniziro cha Kachisi, ndi chifaniziro cha zipangizo zake zonse, momwemo uchimange.