EKSODO 24:17-18
EKSODO 24:17-18 BLPB2014
Ndipo maonekedwe a ulemerero wa Yehova anali ngati moto wonyeketsa pamwamba pa phiri, pamaso pa ana a Israele. Ndipo Mose analowa m'kati mwa mtambo, nakwera m'phirimo; ndipo Mose anakhala m'phiri masiku makumi anai usana ndi usiku.

