Maluko 9:28-29
Maluko 9:28-29 NTNYBL2025
Ndiipo, Yesu yapo wadalowa mnyumba, oyaluzidwa wake adamfunjha paokha, “Ndande yanji ife sitidakhoze kumchocha chiwanda chijha?” Yesu wadaakambila, “Chiwanda ngati ichi sichikoza kuchoka, ingakhale kwa kupembhelape.”