Maluko 7:15
Maluko 7:15 NTNYBL2025
Palibe chindhu chilowa mkati mwa mundhu kuchokela kubwalo icho chikhoza kumchita siwadavomelezeka kwa kumlambila Mnungu. Nambho icho chichoka mkati mwa mundhu ndeicho chimchita mundhu siwadavomelezeka kwa kumlambila Mnungu.