Maluko 6:31
Maluko 6:31 NTNYBL2025
Yesu wadaakambila, “Tiyeni ife tekha pamalo yapo palibe wandhu, kuti tikapumulile pang'ono.” Wadakamba chimwecho ndande kudali ni wandhu ambili kupunda yawo amajha pamenepo ni kuchoka, mbaka Yesu ni oyaluzidwa wake siamakhoze kupata ndhawi ya kudya chakudya ndande ya kwatumikila.