Maluko 2
2
Yesu wamlamicha mundhu wovuwala
Matayo 9:1-8; Luka 5:17-26
1Yapo yadapita masiku yochepa, Yesu wadabwelanjho kumujhi wa Kapelinaumu, wandhu adavela kuti wali kukhomo. 2Wandhu ambili adakomana pamojhi, mbaka padalibe malo yokhala, adajhala pa liwala pa nyumba. Yesu wamalalikila uthenga wa Mnungu. 3Pamenepo, adafika wandhu anayi, adamtenga mundhu wovuwala, adampeleka kwa Yesu. 4Saadakhoze kumpeleka pafupi ni Yesu ndande ya lijha gulu la wandhu. Chimwecho adakwela pamwamba, adafulumula chindu, pajha wadali Yesu. Yapo adafulumula, adamchicha mundhu yujha uku amgoneka pa chitala. 5Yesu yapo wadaona chikhulupililo chao, wadamkambila yujha mundhu wovuwala, “Bwenji langa, nakulekelela machimo yako.” 6Woyaluza akumojhi athauko la Musa, yawo adali pamenepo adaganizila mmitima yao, 7“Chindhu chanji icho chimkhozecha kukamba chimwechi? Wamkafula Mnungu! Ni Mnungu yokha uyo wakhoza kulekelela machimo.” 8Pampajha, Yesu wadayajhiwa yayo amaganizila mmitima yao, wadaakambila, “Bwanji mganiza chimwecho? 9Nichiti chili chopepuka kupunda, kumkambila mundhu uyu wavuwala, ‘Walekeledwa machimo yako,’ kapina kumkambila, ‘Uka, utenge chitala chako upite?’ 10Chipano, nifuna mjhiwe kuti ine Mwana wa Mundhu nali ni ulamulilo wolekelela machimo ya wandhu pajhiko.” Pamenepo, wadamkambila yujha mundhu wadavuwala, 11“Nikukambila, uka utenge chitala chako, upite kukhomo!”
12Pampajha yujha wodwala wadauka, wadatenga chitala chake ni kuchoka, uku wandhu wonjhe niampenya. Wandhu wonjhe adazizwa ni kumtamanda Mnungu, niakamba, “Sitidaonepo chindhu ngati ichi.”
Yesu wamtana Lawi wamchate
Matayo 9:9-13; Luka 5:27-32
13Yesu wadapitanjho mmbhepete mwa nyanja ya Galilaya. Gulu la wandhu lidamchata, nayo wadayamba kuliyaluza. 14Yapo wamapita wadamwona Lawi mwana wa Alifayo, wadakhala panyumba yotengela malipilo. Yesu wadamkambila, “Nichate!” Lawi wadaima nikumchata. 15Yesu yapo wamadya chakudya cha ujhulo pakhomo pa Lawi, wotenga malipilo ambili ni wandhu yawo amajhiwika kuti amachimo adakhala panjhi, amatokudya chakudya ni Yesu pamojhi ni oyaluzidwa wake. Ndande kudali wandhu ambili yawo amamchata. 16Woyaluza thauko anyiawo adali Afalisayo, yapo adamwona Yesu ni wadya ni wandhu amachimo ni otenga malipilo, adaafujha oyaluzidwa wake, “Ndande yanji wakudya ni otenga malipilo ni wandhu yawo ajhiwika kuti amachimo?” 17Yesu yapo wadavela yameneyo, wadaayangha, “Wandhu yawo sadwala siafuna sing'anga, nambho anyiawo afuna sing'anga nianyiwajha adwala. Sinidajhe kwatana wandhu yawo avomelezeka pamaso pa Mnungu, nambho najha kwatana amachimo.”
Yesu walinganicha mayaluzo ya chipano ni yakale
Matayo 9:14-17; Luka 5:33-39
18Oyaluzidwa a Yohana ni oyaluzidwa a Mafalisayo amatomanga kudya. Ndiipo, wandhu wina adajha kumfunjha Yesu, “Ndande yanji oyaluzidwa a Yohana ni a Mafalisayo amanga kudya, nambho oyaluzidwa wako samanga kudya?” 19Yesu wadaayangha, “Bwanji, anyiwajha atanidwa kuukwati akhoza kumanga kudya ni wokwata walipamwepo? Notho, saakhoza kumanga kudya. 20Nambho ndhawi siijhe yapo wokwata siwachochedwe pakati pawo, ni pamenepo saamange kudya.”
21“Palibe mundhu uyo wadula chigamba cha njhalu ya chipano ni kuchisokela kunjhalu ya kale. Wakachita chimwecho, chijha chigamba cha chipano sichiwanange njhalu ya kale, ni yapo pang'ambika sipaonjezeke. 22Chinchijha, wandhu saathila divai ya chipano mmatumba ya vikwetu vakale. Ngati akachita chimwecho, divai siiswe matumba yameneyo, nayo divai siimwazike ni matumba ya chipano siyasweke. Nambho athila divai ya chipano mmatumba ya vikwetu vachipano.”
Yesu nde Ambuye a Siku lo Pumulila
Matayo 12:1-8; Luka 6:1-5
23Siku limojhi lo Pumulila la a Yahudi, Yesu ni woyaluzidwa wake amapita mminda. Yapo amapita, oyaluzidwa wake adayamba kupulula ivo vidali ngati mapila ni kuyapekesa. 24Mafalisayo adamfunjha Yesu, “Ndande yanji oyaluzidwa wako achita chindhu icho sichifunika kuchitika Siku lo Pumulila?” 25Yesu wadaayangha, “Bwanji, simdasome mmalembo yoyela umo wadachitila Daudi pamojhi ni achanjake yapo adali ni njala? 26Mmasiku ya mjhukulu wamkulu Abiatali, Daudi wadalowa mkati mwa nyumba ya Mnungu, wadadya mabumunda yadachochedwa kwa Mnungu, mabumunda yameneyo yamafunika kuti yadyedwe ni ajhukulupe. Nambho Daudi wadadya ni kwaapacha achanjake.” 27Ndiipo Yesu wadaakambila, “Siku lo Pumulila lidaikidwa ndande ya kwathangatila wandhu, ni osati kwachita wandhu akhale akapolo a siku! 28Naponjho ine Mwana wa Mundhu ni Mbuye wa Siku lo Pumulila.”
നിലവിൽ തിരഞ്ഞെടുത്തിരിക്കുന്നു:
Maluko 2: NTNYBL2025
ഹൈലൈറ്റ് ചെയ്യുക
പങ്ക് വെക്കു
പകർത്തുക

നിങ്ങളുടെ എല്ലാ ഉപകരണങ്ങളിലും ഹൈലൈറ്റുകൾ സംരക്ഷിക്കാൻ ആഗ്രഹിക്കുന്നുണ്ടോ? സൈൻ അപ്പ് ചെയ്യുക അല്ലെങ്കിൽ സൈൻ ഇൻ ചെയ്യുക
The New Testament in Nyanja @The Word for The World International and Nyanja Language translation, 2025. All rights reserved.

: