MATEYU 24:7-8
MATEYU 24:7-8 BLPB2014
Pakuti mtundu umodzi wa anthu udzaukirana ndi mtundu wina, ndi ufumu ndi ufumu wina; ndipo kudzakhala njala ndi zivomezi m'malo akutiakuti. Koma ndizo zonsezi zowawa zoyamba.