Logo de YouVersion
Icono de búsqueda

AGALATIYA 6:3-5

AGALATIYA 6:3-5 BLPB2014

Pakuti ngati wina ayesa ali kanthu pokhala ali chabe, adzinyenga yekha. Koma yense ayesere ntchito yake ya iye yekha, ndipo pamenepo adzakhala nako kudzitamandira chifukwa cha iye yekha, si chifukwa cha wina. Pakuti yense adzasenza katundu wake wa iye mwini.